
Kulowa mu Mtendere wa Mulungu
Paulo amatiphunzitsa mmene mtendere wa Mulungu umatetezera mitima yathu ndi mmene tingakhalire pafupi ndi Mulungu wa mtendere.
English: Stepping into God’s Peace
Mvetserani Phunziro la Chingelezi ndi Chichewa
Chiyambi cha Phunziro
Mu gawo loyamba, Paulo akufotokoza zinthu zisanu zofunika kuti mtendere wa Mulungu uyambe kuteteza mitima ndi maganizo athu mwa Khristu Yesu. Mu gawo lachiwiri, amatipatsa malangizo othandiza kukhala mu mtendere wa Mulungu mwa ubale wapafupi ndi Iye.
English lesson introduction
In phase 1, “Stepping into God’s Peace,” Paul uses five necessary qualities to have the peace of God actually begin to guard our hearts and minds in Christ Jesus.
In phase 2, “Abiding in the God of Peace,” specific guidelines are provided enabling us to see how to live in God’s peace by our closeness with Him.