Gawo Loyamba — Okhulupirira Atsopano
Okhulupirira atsopano amafunikira kutsimikizika kwa chipulumutso, kudziwa Mulungu monga Atate, ndi kuthandizidwa kukhazikitsa maziko olimba a moyo wauzimu.
English: The basic needs of new believers and how the church can care for them well.
Onerani ndi Kumvetsera
Phunzirani ndi Kugwiritsa Ntchito
- Kodi magawo atatu a kukula kwa Mkhristu amene Yohane akunena ndi ati?
- Kodi Yohane akunena chiyani kwa okhulupirira atsopano mu 1 Yohane 2:12–14?
- Ndi zizindikiro ziti za gawo loyamba la kukula kwa Mkhristu?
- Ndi mavuto ati amene okhulupirira atsopano amakumana nawo?
- N’chiyani chiyenera kuchitika pa gawo limeneli?
- Kodi chingachitike n’chiyani ngati okhulupirira atsopano salandira chithandizo choyenera?
- Kodi munaphunzitsidwa bwino pamene munali wokhulupirira watsopano?
- Kodi mwathandizapo ena pa gawo limeneli?
English study questions
- What are the three stages of Christian growth that John describes? How do these form an analogy for the physical development of a person?
- List the items that the elderly apostle says to this first level of believers? Look in 1 John 2:12-14. Be specific.
- What characterizes this first stage of the Christian's growth?
- What are the problems or challenges that those in this spiritual stage will face?
- Summarize what is suppose to happen in this stage of spiritual growth.
- What might happen if Christians in this spiritual stage do not get the needed support? Be specific.
- Are you in this first stage? Were you discipled.
- Have you discipled others.
Podikasiti: Phunziroli likupezekanso mu Maphunziro a Chikhristu mu Chichewa.